ANMELDEN
EINLOGGEN
The Very Best - Mwazi [Blood] Songtexte
Startseite
T
The Very Best
Mwazi [Blood]
Ukakhala iwe mphwanga
Usadzinamize uli ndi abale
Amakukonda uli ndi chuma
Ukasauka kukutaya
Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
Umawundana kuposa madzi
Iwe iwe mvera
Tchera tchera khutu
Ganiza ngati munthu
Dieser text wurde
259
mal gelesen.
The Very Best
Songtexte