KBG - Zoononga Moyo Lyrics

Verse 1:LAWI
Amati bawa
ndi njira yochotsela nkhawa
nanga bwanji ukadzuka mmawa
matsile maluzi uliso confused
ndingonena chindunji
chenicheni nchiti
chokhalila mfiti
when in actual sense you r a slave to the sin that yo glue to
iwe tchimo litavala umunthu
chonde ndithandizeni
ndidziweko swaga as much as i know ndizoononga moyo wanga
sikuzikweza kodi?
Kuwalila kodi?
Kukhutitsidwa ndimmene ndavalila kodi?
Inde asungwana apapa mukukhwana titha kuyamikila mpakana kupanga mwana
Inde abwana mwatchena osanama but check on the . . . Ndiyesu mwasemphana
u can be who u want to b
multiply zinthu ngati tyms
u can buy evrything with paper
but heaven uuuh uuuh zachisoni pepa

{Chorus:}
kodi wapindulanji iweyo
utapeza zonse zofuna mtima wako
koma zonse zomwe wapezazo
mulibe chipulumutso
ndizinthu zoonona moyo wako x2

Verse2:KBG
lawi nane ndiwauze fanzi
. . . .
This lyrics has been read 317 times.