注册
登录
The Very Best - Mwazi [Blood] 歌词
主页
T
The Very Best
Mwazi [Blood]
Ukakhala iwe mphwanga
Usadzinamize uli ndi abale
Amakukonda uli ndi chuma
Ukasauka kukutaya
Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
Umawundana kuposa madzi
Iwe iwe mvera
Tchera tchera khutu
Ganiza ngati munthu
这个歌词已经
264
次被阅读了
The Very Best
歌词